lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu i-starn 08 - god's love

Loading...

(intro)
audiowave, it’s gon’ be a bang!
take them high boy!

(verse 1: i~starn 08)
ndikagwa
mumandidzutsa
ndikasochera
mumandibweza
ndinu mulungu wadzulo, lero, mawa simusintha
chikondi chanu
ndichopanda malire
mwandikondera muzinthu zambiri
mwachoka nane kuja ndi kutali
pandekha sin’kanafika apa
ichi ndichisomo chanu mbuye
mwandichotsa mumatope
kundisambitsa kundivekaveka
i got nothing to complain
this is unconditional love
chisangalalo chosatha muntima
’cause his love never fail me
iwe suntha, ndipatse mpata
i wanna dance for jesus
chisangalalo chosatha muntima
’cause his love never fail me
iwe suntha, ndipatse mpata
i wanna dance for jesus
(chorus: i~starn 08)
ndinu mulungu wadzulo, lero mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
mbuye ndinu mulungu wadzulo, lero, mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
ndinu mulungu wadzulo, lero mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
mbuye ndinu mulungu wadzulo, lero, mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire

(verse 2: kamag~nius)
hebrews 13, verse ya 8
yesu khristu ali yemweyo
dzulo komaso lero ndiku nthawi zonse
pamavuto, pantendere
iye sangatinyoze
iye sangatinyoze
i’m a son of god i’m not lonely
my father in heaven is holy
mulungu wa abraham
mulungu wa abraham
mukondana nawo onse ok~mverani
yehova…..

(chorus: i~starn 08)
ndinu mulungu wadzulo, lero mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
mbuye ndinu mulungu wadzulo, lero, mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
ndinu mulungu wadzulo, lero mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
mbuye ndinu mulungu wadzulo, lero, mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
(verse 3: t~nam)
god’s love is the best love
there’s no love like his love
his faithful is forever
he’ll always be there whenever
my life is in his hands, he’s there when i need him
an ever loving god
he’s an everlasting god
ndidzamutamanda yehova
ndidzamuthokoza yehova
poti iye ndi amene andisamala nthawi zonse
timukwezeke yehova
timuyamike yehova
poti iye ndi amene
atisunga ife tonse

(chorus: i~starn 08)
ndinu mulungu wadzulo, lero mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
mbuye ndinu mulungu wadzulo, lero, mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
ndinu mulungu wadzulo, lero mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire
mbuye ndinu mulungu wadzulo, lero, mawa simusintha
chikondi chanu, ndichopanda malire

Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...