lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu hp - la la la

Loading...

{verse 1}

ndikakhala ndiwe sindidandaula ine vuto palibe
ndimafila bwino china chilichonse ndiwe ndingakwanitse
ugwire w~nga mkono ukhale nane pompa, nthawi zonse ukhalebe
dziwa zanga zonse ndazipereka monse mw~nga m’mwaiwe

{hook}

oh wachikondi waine
palibe wina pa iwe
ugunda mtima waine umveka la la la la la la la
utenge zonse mwaliwe
zanga zonse ndati ine
ugunda mtima w~ngau umveka la la la la la la la la la la
la la la la la la la
la la la la la la la
la la la la la la la
la la la la

[verse 2}

you know that i don’t care
all i want is to stay
by your side baby
yeah you drive me crazy
you know that i don’t play
all i want is to stay
in your heart oh lady
we should be…..

oh take my hand and let us dance
give me yours i’ll givе you mine
you are my angel
you arе my angel yes

{hook}

oh wachikondi waine
palibe wina pa iwe
ugunda mtima waine umveka la la la la la la la
utenge zonse mwaliwe
zanga zonse ndati ine
ugunda mtima w~ngau umveka la la la la la la la la la la
la la la la la la la
la la la la la la la
la la la la la la la
la la la la


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...