lirik lagu gwamba - akondakitale
[intro: lawi]
yi, aye~iye~yah
aye~iye~yah
[chorus: lawi]
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje

ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 1:gwamba]
aish, ndalama nde yavuta pa nyasa
daily fans k~mayisaka
sikuwona zoti ndiwe shasha
k~menya business basi k~mayitsatsa
nde mukapeza ka ndalama sister, chonde k~makagwiritsitsa
mukamagona nako kukafunditsa
kwachuluka mbava nde muzikabisa
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w~ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 2: gwamba]
aish, conductor pokwera umati 100 ndangokhala pansi ukuti 120
aseh, osaziyamba zin~z~
muno sindichoka ngati sundipatsa change
wekha ukudziwa dollar ili pa minga
povaya kudedza pena kukwera njinga
umayesa ngati ukundiyimba
lero lonkha wandilira sindiyimva
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w~ngondivuta ndi uphawi (ayi)
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje
inu ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
[verse 3: gwamba]
aish, komanso yesu akufuna change mama
koma change akufuna iye si ndalama
akufunitsitsa inuyo makamaka mutasintha ndikuyamba k~mutsata
mapemphero ndi hustle ya uzimu
mukapusa tsiku lomaliza, no change
mapemphero ndi hustle ya uzimu
ukapusa tsiku lomaliza, no change
[chorus: lawi]
yi, ndikupempha mundithandize
yi, w~ngondivuta ndi umphawi
ah, ah
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
akondakitale ndalama ndalipilayi ndati ndipemphe, mundibwenzereko chenje
ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko change
inu ulendo w~nga ukathera ku lilongwe, m’deport
koma ndipemphe, mundibwenzereko chenje, yi
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu don said - send nudes
- lirik lagu noa azazel - dreaming alone
- lirik lagu vic mensa - murderface
- lirik lagu various artists - happy, happy birthday to you
- lirik lagu the who - time is passing (live at the young vic, london, 26 april 1971)
- lirik lagu randy savvy - lone ranger / faxxx
- lirik lagu quest the journey - mind
- lirik lagu zoe wees - hold me like you used to (paul woolford remix)
- lirik lagu mike pender's searchers - walk in the room
- lirik lagu emotionplug - intro (dialogue at daybreak)