lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu guntolah - ndikuzizimusani

Loading...

oops on the board
louder
kupeza omukonda ndikhala pa low, pachuluka afiti pa mudzi pano
kupeza ka dollar ndikhala pa low
anthu akangoziwa ngini yanga ili bho, ati wazitenga kuti uyu
wazitenga kuti
wazitenga kuti uyu, wazitenga kuti

mukauzane aah mukatutane ah
mukauzane aah mukatutane
osatila moyo w~nga mma status, ndikuzizimusani
akadziwa zikuyenda aku hater, ndikuzizimusani
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

angodabwa save the date, angodabwa ndili ku states
angodabwa save the date, angodabwa ndagula benz
paja munandipasa malire, izi singafikile
paja munandipasa malire eeh, singafikile

mukauzane aah mukatutane ah
mukauzane aah mukatutane
osatila moyo w~nga mma status, ndikuzizimusani
akadziwa zikuyenda aku hater, ndikuzizimusani
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)
sangaononge chinthu chomwe sachiziwa
ndisanatchuke anthu asanandidziwe
zanga zinkandiyendela, mbuye ankandikondela
olo babe yanga simmene inkandikondela
koma dalitso wina umabwela ndi ziphinjo
nthawi yopemphela ndik~makhala ku show
anzanga anachuluka sindikhala pa door
satana naye ali busy kuti andimalize
poti za moyo w~nga akuziziwa mwa easy
ndeno ndapanga chi sankho, kuti ndizipatule
ena aziti ndi sankho
ndikuphusha hustle apa ndinagula passo
sindinena chikubwela koma anthu azizwanso

mukauzane aah mukatutane ah
mukauzane aah mukatutane
osatila moyo w~nga mma status, ndikuzizimusani
akadziwa zikuyenda aku hater, ndikuzizimusani
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)
ndikuzizimusani yea ndikuzizimusani (ndikuzizimusani)

Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...