lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu eli njuchi - ondi

Loading...

[intro]
savage

[verse 1]
amakondwa onse akandiona, ondilandira ine
chimwemwe ndi ziweto zomwe, ondilandira ine
ndili ndi ana ondichingamira ndikafika ndikanakonda akandione (ndikanakonda akandione)
kuli abale omwe andisowa komwe ndilinjikaku
ndinakakonda akandione (ndikanakonda akandione)

[chorus]
imani nditsike, tsike, tsike, tikuthamangiranji?
tikuthamangiranji yea
kuli bwino ndiyende, yende, yende, tikuthamangiranji yea
tikuthamangiranji yea

[verse 2]
a dalayvala imani kaye eh heh, ndati ndifunse nawo
mu galimoto muno, mu bus muno wachedwayo timudziwe nawo?
tikuthawanji? speed mpaka two hands mseu wake uti?
ma overtake osaona kuti kuli bwanji, mseu wake uti?
ndeno kupewa kuposa kuchiza
sumutamika mukatigwetsa
kuli bwino tikafike mochedwa osati ma bandagewo titamangidwa
kuli abale omwe andisowa komwe ndilinjikaku
ndikanakonda akandione, wa moyo akandione
[chorus]
imani nditsike, tsike, tsike nanga tikuthamangiranji? yea
tikuthamangiranji?
kuli bwino ndiyende, yende, yende, tikuthamangiranji? yea
tikuthamangiranji?
imani nditsike, tsike, tsike nanga tikuthamangiranji? yea
tikuthamangiranji?
kuli bwino ndiyende, yende, yende, tikuthamangiranji? yea
tikuthamangiranji? yea

[outro]
yeah
tikuthamangiranji? tikuthamangiranji?


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...