lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu eli njuchi, chizmo sting & veda njuchi - asa

Loading...

[intro]
savage
savage (njuchi)

[verse 1: eli njuchi]
mantha amachoka anawa, akamandiona
amadziwa pali soja anawa, akamandiona
khumbo langa apapa, ndipempha mundichize
kuti chonde ana angawa (asa), asadziwe
ma injury a soja, ma injury a soja awa (asadziwe)
zoti pena ndimalema zamabala amu mtima awa (asadziwe)
ma injury a soja, ma injury a soja awa (asadziwe)
zoti pena ndimatopa, nane ndi munthu ndimaf~~ka awa (asadziwe)

[chorus: eli njuchi & chizmo sting]
asadziwe (asadziwe)
zomwe ndimawona, zomwe ndimaona apa (asadziwe)
asadziwe (asadziwe)
(mabala amu mtima, mabala amu mtima awa) (asadziwe)

[verse 2: chizmo sting]
asadziwe ndimadutsa mu zikh0m~
bread ndima winira zisomo
ndikafika kulandiridwa pa kh0m~
ndi mangoti ambuye zikomo
i sacrificed my nights for them to see a brighter day
i done fight my fights just to see dem smile at me (oh, oh)
ma injury a soja, ma injury a soja awa
pena ndimalema koma ndimangozisunga mu mtima (oh)
ma injury a soja, ma injury a soja awa
asadziwe onsewa jah wa , asadziwe onsewa jah wa
[chorus: eli njuchi & chizmo sting]
asadziwe (asadziwe)
zomwe ndimawona, zomwe ndimaona apa (asadziwе)
asadziwe (asadziwe)
(mabala amu mtima, mabala amu mtima awa)

[verse 3: vedda njuchi]
koma the way how wе do it jah
samadziwa amangowona zachitika
timavaya through sweat before sweet
filimu ndi yanga koma sine akita
samadziwa ndimvera ine, kona kusangalala zomwe ndifuna ine
nkhondoyi sindingawalore kuti ajoine (shh)

[outro: eli njuchi & chizmo sting]
(ma injury a soja, ma injury a soja awa
oh, yeah, yeah)
(njuchi)


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...