lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu dirty flo - yolakwa (skit)

Loading...

[intro: krazie g, dirty flo & lil al]
ati iyeyo ndi f~f nine
yeah dirty yeah
nde ndinak~mana ndika baddie kenakake
nde nangokawonetsa naneso ndi bad news
(timothy got the fire beats no matter what it is)
wagwan, wagwan chinachake
yeah content yoti, dikila umve mene inayendela eti

[verse 1: dirty flo]
anthu awiri sangayende, asanapangane
real recognize real yeah, deal inapita kwa deal
kanzake kofatsa komabe sitikudziwa zomwe k~mbali amakamvana
innocent looks koma samaphana ndi ana
kuthoka mophweketsa ati “uzapakula ukakula”
ati ndi woyendayеnda ndati “naneso ndili paduwa”
uh uh ukuyankhulitsa ndi vumbuluke ndingoying’alula
ine ndi yolakwa kalе nthawi yochongetsa ndizibanduka

[chorus: dirty flo]
ngati yalakwa pa den ine sik~malakwa pa den
ngati ukupanga za geli part time ndi plenty
nditha kupatsa test tiye tidyere limodzi
chif~kwa tikufana taste tonse yolakwa
yolakwa, yolakwa imayenda yolakwa
yolakwa, yolakwa yatengana yolakwa
yolakwa, yolakwa imayenda yolakwa
[verse 2: dirty flo]
ndikadolo choncho tikuyilakwitsa titavala ma nike sneakers
kuzifila kudziwa she like “i know all you n~ggas”
i’m like “i know you sisters”
atha kulowa onse azinzakowo
ino ndimayilakwitsa sidzadza
amawona ngati ak~mwa wine
nda mixer zi shooter ndi two spitter basi

[outro]
haha
timothy got the fire beats no matter what it is
oh zinthu zakezo ndi zotere


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...