lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu dirty flo - manja lende

Loading...

[intro: krazie g & lil al]
ati iyeyo ndi f~f nine
yah ay, ay

[verse 1: lil al]
fresh outta, fresh outta
ndine shatta, ndine shatta
side chick kakapempha gist ndik~mupatsa
kape akapempha bean ndik~mana
iwe uzihasser, uzihasser
wosowa ya mogo sangagule mpasha
zimafunika fanzi yoti imazitsata
sanga runny dancehall olo utawapatsa mpata

[chorus: dirty flo & lil al]
yeah
manja lende kusowa pogwira akamadzuka
asapemphe osamulora ak~masuka
tisamtenge akungotha malo sitipindula
sitngacheze ndili ndi zochita ndikubanduka

[post~chorus:dirty flo & lil al]
manja lende,yeah sitingacheze
iwe manja lende, ngati~
iwe manja lende, sitingacheze
iwe manja lende, sitingacheze (manja lende, lende)
yoh
[verse 2: dirty flo]
manja lende mbola sangakhale munyane
manje lende k~mboyu koma sangandikankhe
salimwendo ugwile liam[?] one step ahead (step ahead)
ndinavutitsa ndili mwana kafunse a head (afunse a head)
manje lende ndine sitinganyamuzane
kulibwino ndingonyamula ndekha ma man
son of a gun ine mwana bullet (pha! pha!)
zakulemerani izi tikutuleni

[chorus: dirty flo & lil al]
manja lende kusowa pogwira akamadzuka
asapemphe osamulora ak~masuka
tisamtenge akungotha malo sitipindula
sitingacheze ndili ndi zochita ndikubanduka

[post~chorus:dirty flo & lil al & don sw~nky m. i. b]
manja lende,yeah sitingacheze
iwe manja lende, ngati~
iwe manja lende, sitingacheze
(energy, energy, energy) iwe manja lende ,sitingacheze (manja lende, lende)

[verse 3: don sw~nky m. i. b]
ndine sw~nky ndimathangitsa filo
ndili high jomabe ndine lilot
m. i. b is not for men in black
m. i. b is for the money in the bank
hustle hard is what i do ebryday
if you gettin’ lazy you can’t chill with us anyway
watopadi motivation sungayimve
zosanonadi koma sungadye za ife
[chorus: dirty flo & lil al]
yeah
manja lende kusowa pogwira akamadzuka
asapemphe osamulora ak~masuka
tisamtenge akungotha malo sitipindula
sitngacheze ndili ndi zochita ndikubanduka

[post~chorus:dirty flo & lil al]
manja lende,yeah sitingacheze
iwe manja lende,ngati~
iwe manja lende,sitngacheze
iwe manja lende,sitingacheze (manja lende, lende)


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...