lirik lagu dirty flo - kulira
[verse 1]
pali left, right, pali black ndi white
utha kukhala ku front utha kukhala behind
utha kukhala dead utha kukhala alive
utha kukhala ndi fear utha kukhalaso brave
ukhoza kukhala ndi friend akhoza kukhalaso m’dani
ukhoza kukhala ndi uncle koma awa kufunsa ”ndi ndani?”
pafunika ziwiri tisiyanitse, ziwiri kuti tisalimbirane
tenga mbali yako sungakhale zonse
ichi changa chako chili pati?
[pre~chorus]
zina kamba zina leku
zina mtendere zina ndeu
ukamva kulira kwa satana ndi chimwemwe pamaso pa mlengi w~nga
[chorus]
ine ndine ndikulira kwa hater w~nga koma ku fila kwa fanz yanga
ndine kufila kwa mg1 koma kilira kwa ma baddie
zilengo ziwiri zimangolandirana
kuchoka mdima kukacha kuwala
olo zikakukulira mtume mwana
kukagwetsa pansi kuti kazilira mwamba
[verse 2]
yeah, ay
olo malo alipo mkati ndi panja
pali zibwenzi palinso ma banja
mukanyika ife tizakuvuwulani
mukabisa ife tizakululani
yeah, ana a lero ndinu kulira kwa ana a make dzana
rastaman ndiwe kulira kwa barberman
sungamangolandira uzipeleka
ngati iwe siwе wolankhula ndekuti ndiwe womvera
class yamwa, inе ndikukhuta pa plug
mthumba mw~nga mwa kwiya ndikusunga zi dollar ku bank
kakuyitana vaya usakapezeka tavala
olo kakabwera kakuyenera kazivaya
ma fellow ena amandipatsa ma farewell
kundipatsa zero nk~matu ndi a circle
kulira kwa satana ndi chimwemwe pamaso pa mlengi w~nga
yeah, straight outta ll’z i’m keepin’ it g
amakupatsani za ulere, ine ndikulipiritsa
usathamamge magazi usanaone drive
yomwe ndik~mayendera nde muli engine
dikira uwone wekha umva iwe
[chorus]
ine ndine ndikulira kwa hater w~nga koma ku fila kwa fanz yanga
ndine kufila kwa mg1 koma kilira kwa ma baddie
zilengo ziwiri zimangolandirana
kuchoka mdima kukacha kuwala
olo zikakukulira mtume mwana
kukagwetsa pansi kuti kazilira mwamba
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu naelis - no me toques el corazón
- lirik lagu kind beast - in it to win it
- lirik lagu famille nombreuse - j'parle vrai
- lirik lagu demi lovato, zoe gitter & alex chapman - kiss (gag remix)
- lirik lagu primetae madiadi & jaitekken - cleopatra*
- lirik lagu bill nelson - a kind of loving (the stephen w. taylor remix)
- lirik lagu lady yeska - me los fumo
- lirik lagu bigguccidame - no danny phantom
- lirik lagu soyupoyu - staytion
- lirik lagu tatsei - cyberpsychosis