lirik lagu crispy malawi - ngati ine
[chorus]
utha kupeza wina koma sungapeze wina ngati ine (like me, like me, like me)
utha k~mamvana naye koma sungamvane nzomwe umvana ndi ine
sine wanna be, life yanga ndima liva ngati ine
pano mafana amaimilira akafuna kukhala ngati ine
[verse]
mesa ndukuuza nangobadwa chonchi sinachalire (i ain’t forcing a bov trait)
amangondimva nde zongva kupwetekesa mutu matsire
ndine spe chingaipe sine maskal usadalire
you know i’m married to money nde chibwezi chathu sichingalimbe
dzulo btz lero ndiku mzuzu
ofunika dhen ku kasungu ngati kamuzu
tili mu kitchen busy cooking ngati pun kasusu
(malawian) chichewa chik~mveka ngati chizungu
ati “spe kodi walеmba kapena zungochoka mmutu”
if it wasn’t for this album nakangolemba buku
pena ndimazimva ngati ndaziika ku nkhutu
abalе si t shirt ndi a’ba.lé ndi mtundu community
sitikulenga ngati ma guy praying for more life ndi financial stability
the price went up mix nedzability
funika more than 1 mita sindimaimba za charity
[chorus]
utha kupeza wina koma sungapeze wina ngati ine (like me, like me, like me)
utha k~mamvana naye koma sungamvane nzomwe umvana ndi ine
sine wanna be, life yanga ndima liva ngati ine
pano mafana amaimilira akafuna kukhala ngati ine
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu villemdrillem & karl killing - kaotan
- lirik lagu thabang! - hark! the telescreen(s)!
- lirik lagu tana - finsta
- lirik lagu cuteteeth14 - halloween fest @ cute teeth14
- lirik lagu akethesis & pl0hbshk - d4rk r00m
- lirik lagu 59blum - devil
- lirik lagu murphy me - first pick
- lirik lagu venny sianturi - jangan pergi, sayang
- lirik lagu ada rook - shooting siblings
- lirik lagu creeper - the crimson bride