lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu crispy malawi - interlude

Loading...

[intro]
cheo meek hiihihi
you know
yeah
turn it up
malawian
welcome back blake
mhu

[chorus]
rest in peace to patricia
all i ever wanted was a mic ndi chi mixer
pano ma gee akafuna feature ndimalipilitsa
ena ndimawawaza ena ndimawakwiyitsa
eh i love my girl kungoti talandira ndi eliza
nditha kutchola door just to get bros inside
ndilipa pa mirror like h~ll yeah i’m that n~gga
we in the music business a diddy
ndi achina jigga

[verse]
remember how started ngati za jokes
kupanga record after school ndi achina paul
now we moving city to city kupanga ma show
money ipange flow, tikhale bho bho
ndimakhala busy mami ndimatanganidwa
ndiku runner new wave ku malawi ntanganywika
kuthamangitsa gist koma osathamangira
kuvutitsa pa stage ngati mfana woyitanira(akwere nawo ya m’town)
ha
rest in pеace fati khaza[?]
ndikudziwa wa hitter kale stu
ndi achina martsе nkhata
kuwonetsa action mafana omangobwata
kuwapatsa chochita ana oti amangokhala
huh
rest in peace to my feelings
ma babe osa pusher ine sindingakufileni
undipeza ku stu ine mfana wa ku dm
album on the way ndipatse sp~ce eh clear(sp~ce)
[chorus]
rest in peace to patricia
all i ever wanted was a mic ndi chi mixer
pano ma gee akafuna feature ndimalipilitsa
ena ndimawawaza ena ndimawafilitsa

[outro]
(achina yeah)
(yeah eliza)
(nditha kutchola door just to get bros inside)
(kutchola chitseko)
(ndilipa pa mirror like h~ll yeah i’m that n~gga)
(we in the music business ngat jigga)
(ndi achina spe)
cheo meek hiihihi mhuu


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...