lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu crispy malawi - gu gu gu

Loading...

timothy got the fire beats no matter what it is
ayo landie
[hook: crispy malawi]
ukamva gu! gu! gu! gu speaker yakwa neighbour
gu! gu! gu! speaker yakwa neighbour
gu gu! gu! speaker yakwa neighbour
ukamva!

[verse 1: crispy malawi & brainlock jeff nyimbo]
slatt
kwabwera smokey ndi themba..
samaona kuti lero ndi lolemba
kungodya ma zaza ntibu tangokweza
playlist ya dj neighbor suzayiloweza
chotsa ti nyimbo tako faka crispy ndi krazy
za alamu anu ukamufunse celba ndi zeze
brainlock in the mix itsitse ikweze
ndili ndi chi keys chi jeff isokoneze

kwathu k~mveka nyimbo
kwa neighbour k~mveka nyama
chispeaker kukopa fanz amayesa ngati ma scammer
the way i do my dance ngati mc hammer
speaker tangokweza nde today mu runner
ndikudya ka loud sound ili low
ayy
tandipatse cow kuti ndivine ngati nyau
she send me little letter
she says she’s getting better
i’m never under pressure
chi speaker ndangokweza
[hook: crispy malawi]
ukamva gu! gu! gu! gu speaker yakwa neighbour
gu! gu! gu! speaker yakwa neighbour
gu gu! gu! speaker yakwa neighbour
ukamva!

[verse 2: brainlock t~kas & brainlock kizmet]
speaker yakwa neighbour indiboola makutu
kungochoka vep akut speaker ituluke
ungodina next uwone akutulutse
kuti gu!gu!gu!gu! mpakana kuche
kukanika kubleya man
ma window kutseka blaz
azimayi kuchola dance,ma babe ku twerka man
muno ndimu hood mw~nga wina andinyumwitse
yesa zida phw~nga uwone fanz ikuwukire
neighbour ziphokoso
ndi yambisa nkhondo
ndivaya ku popo
ndivaya konko
neighbour ziphokoso
yambisa nkhondo
vaya ku popo
vaya konko

ah speaker yakwa ikati isokosere
imakhala full blast basi asokoneze
ndichi ntibu makina chimphaso makoswe
koma de~fra basi ndiyi bongose
daily kwa neighbour ngati kuli ma demo
iwe kufa makutu ngati wasonkha ya memo
neighbour samamva za munthu
iyeyo ndi wa ghetto
speaker yake inathawa nawo mazeno
[bridge : brainlock kizmet]
neighbour neighbour umatiwonjeza
neighbour neighbour pajatu ndinalonjeza
koma tangowona sound yako wayikweza
neighbour neighbour
neighbour neighbour suzatheka

[verse 3: brainlock kushizo & brainlock boi sticx]
ndazuka chif~kwa cha noise
speaker yakwa neighbour imeneyo
ingolongola w~ngokweza zima 808
wayamba chama quarter to
pano ili past two
ndikungomva gugugu wandisokoneza mutu
iwe neighbour bwanji ukukweza sound ngati ndi december
wayamba kale kale kuthoka sukuleka
sound ili loud ngati zaza ndi kukhwemba
umandijayila tsiku lina ndizakukwenya
uzandimva ndikanena
pano sumakhala wekha
makufila ndiwe neighbour
koma nzakutopela
ndikabwera kupeza sound wakweza
kuli ana akufuna kubleya

speaker yakwa neighbour imandisokoneza guys
zoti ndimableya ndangodzuka ku roller spliff
ti ana tingodabwa kodi ali kut sticx
moto sung~yake opanda iyeyo calling[?]
ndinali ku pharmacy kugula kaye madzi
themba ali ndi sprite crispy ali ndi zaza
magetsi akathima neighbour ali ndi generator
zoma flexer ka mwana kake amandiletsa
koma boys sizamva ndili naye ku corner
eko ka ganja kali cheche ta roller[?]
kuwona speaker ngati ma sister ku culture[?]
nditha kukagona konko mpaka kukacha


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...