lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu crispy malawi - angobwerabe

Loading...

[intro]
f~f9ine

[pre~chorus]
ma babe ambiri man angobwerabe
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party

[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik~mane
sitik~mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade

[verse 1]
nnamukwera kale sanganditsike
ati ali ndi guy oti sangamu cheaty
ex w~nga wina anagwidwa ndi dj
koma ntafuna nditha k~mu caller kuti ndimu~
k~mudeleter ngati amangooneka bho pa ma pictures
ama roller ndi adani k~mawauza kuti andidisse
nnangoziwa kuti si level basi k~mandipanga compare ineyo ndi achina piksy
iwe, yachina spe ndi 1 of 1 sungamafananize
sindingakunamize, ngati sufila dancehal sindingakukakamize
nditha kushala nawe koma sindingakhalitse
umuuzenso blesser wako ndikugulisa ma lipha ndi ma t shirt
osamaphwеkesa mission
[pre~chorus]
ma babe ambiri man angobwerabе
43, chimaliro , nyambadwe
ena ali single ena umake
ali ndi a eniake
ali single ngati ali ku party

[chorus]
ali single ngati ali ku party
akufila ati tik~mane
sitik~mvana ngati sitingadyane
ofila dancehall sangamanyade


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...