
lirik lagu crispy malawi & dirty flo - wakuba (interlude)
[intro: dirty flo]
aku recorder ndi yashie
iwe aku recorder ndi yashie
iwe aku recoder ndi yashie
[pre~chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak~mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k~muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
[verse: crispy malawi & dirty flo]
k~mu caller dirty ati iyeyo ali kwa duda
kuyithoka boys yanga ati samasuta
koma amazanditenga kuvaya kwa plug koma kusonkha yamafuta
ndimadya ndine koma kungoti ghetto simakhuta
malo si ake koma ndadabwa wamasuka
attention yanga sinduyiwona ndani wasunga? (yeah)
atha kubela mpweya iwe ndikubanika
ofunika k~mu searcher uyu akamapita (mh)
(yeah, yeah) nde akamavina mpamene umaziwa kuti ass yangodzadza ndi ma fats
amangokwiya ati ndimachulutsa ma facts
pa tiktok ndimafila f~kwa ali ndi chi nyash
olo mbina ndamudabwa mene wanyamulira
waba uku koma uku nkomwe wajudukira
timuphika f~kwa watibela chopakulira
waba moto fanzi ikuwona ngati wazimitsira
[pre~chorus: crispy malawi, dirty flo, both]
wakuba
amawoneka woyera koma ndi mkazi wakuda (eh)
mkazi wak~mpanda koma looks ndipanja wakunja (yea)
olo k~muloleza amatenga mwakuba
koma ali safe ali m’manja mwakuba
[chorus: dirty flo, dirty flow & crispy malawi]
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
uyo, uyo, uyo, uyo, wakuba
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu humberto & ronaldo & ícaro e gilmar - pensa bem (ao vivo)
- lirik lagu lil hope 3x - corrupt 2
- lirik lagu honeymoon arcade & sillage - i hate it when somebody says your name (remix)
- lirik lagu gönül akkor - onun nikahı bende
- lirik lagu the planet smashers - things you do
- lirik lagu prynce geno - double decker
- lirik lagu klangkuenstler & ski aggu - sonne geht auf
- lirik lagu the tree of wisdom & the wiggles - shed, mower and a boat to tow
- lirik lagu thecomputernerd01 - 2010 rap
- lirik lagu rəssam & araz rafail - səndən bir istəyim var