lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu clovix - sake

Loading...

eh

eh…. 

mwana  usadande (aaaah)
mwananga usadande
eh mwananga usadande

mi  work hard 6 to 6 (for your sake)
k-mangidwa  ndi a police(for your sake)
kupangaso risky business (for your sake)
fighting  that one makes you stress(for your sake)
hustlin all day n night (for your sake)
staying awake late @ night (for your sake)
everything for you baby (baby)
just  fi yah good life baby

for your sake oh lelelele….(my baby)
for your sake oh no eh….(x2)

ofcourse singathe kupanga zonse (baby) koma sindingaleke (baby)
kugwira ntchito molimbika zofunika everyday zipezeke
singathe kukupatsa ine zonse(baby) koma sindingaleke(baby)
kugwira ntchito molimbika someday khumbo lako lizatheke

working hard 6 to 6 (for your sake)
k-mangidwa ndi a police (for your sake)
kupangaso risky business (for your sake)
fighting that one makes you stress (for your sake)
hustlin all day n night (for your sake)
staying awake late @ night (for your sake)
olo nditadwala sindimafokabe
mi still hustle hard

as long as i live
ndiziyetsetsa mbali yanga kuti uzikhala okondwa
as long as i live
ndikulonjeze mwana w-nga moyo mwako sinzachoka
pena ndimakukhumudwitsa
udindo w-nga simaukwanitsa
nane ndine munthu ndili ndi zof–ka
but fi yah good ndiyetsetsa osafoka

for your sake oh lelelele….
for your sake oh no eh….(x2)

ofcourse singathe kupanga zonse koma sindingaleke
kugwira ntchito molimbika zofunika everyday zipezeke
singathe kukupatsa ine zonse koma sindingaleke
kugwira ntchito molimbika someday khumbo lako lizatheke

working hard 6 to 6 (for your sake)
k-mangidwa ndi a police (for your sake)
kupangaso risky business (for your sake)
fighting that one makes you stress (for your sake)
hustlin all day n night (for your sake)
staying awake late @ night (for your sake)
olo nditadwala sindimafokabe
mi still hustle hard

for your sake lelelele….
for your sake oh no eh…

….the end….
artist : clovix
song : sake
produced by taktic (frame city rich)

a 2019 karbon clan & the tag team presentation


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...