lirik lagu brainlock t-kas & nkhiwa - suprised
[intro: brainlock ~tkas]
woo
[chorus: brainlock ~tkas]
if you really know me
then you wouldn’t be surprised
daily ndimazisaka sindif~~ka ma guy (no way)
thanzi paliponse sindingasiye kudya nazz (ayy)
ati ndi ine shasha ndamufunsa wadziwa bwanji?(wadziwa bwanji?)
ati uli ndi drip ngati mvula (ngati mvula) (ayy)
ukakondwa umavuta (ukakondwa umavuta) (ayy)
ex wako amakufuna (amakufunabe iwe) (ayy)
umanjoya opanda chuma (uh huh)
[verse 1: brainlock ~tkas]
drip yanga ndi lo lol ol ndabwera ndi nkhani (okay)
push to start slatt slatt i was in a rush (uh huh)
magobo kwambiri usadabwe ndilibe nthawi (ndilibe)
pano ndi pa town sundifuna kufa mphawi (kufa mphawi) (nah)
trap trap trap moyo wako usanagonje (trap)
mweratu zi pints
blazer zi ganja, imwa zi nyombe
uvaye ku church za mlengi usaf~~ke (amen)
akakuwopyeza thila fire usaope (krr pow)
mmh
pano stizz inasintha (oh yeah)
ife tilipa top palibe kutsika (palibe)
snakes in the grass kutchetcha kapinga
[verse 2: nkhiwa]
(stumbo!)
you wouldn’t be surprised ngati iweyo umandiziwa;(umandiziwa)
kubwera ndi good vibes ex wako akudziwa (akudiziwa)
trap yanga ndi ya standard (yeah)
no room for the muf~ckin’ blunder (blunder)
trap yanga ili hot simadikiraso summer (aah)
yeah v~a~p~e in your face (in your face)
yeah tonse ndife themba timangosiyana face (kusiyana face)
ti afana azi nyombi tingo dropper zima verse (ma verse)
i’m with the taliban enough is not worse (ayy)
we stay on top (we stay on top)
we stay climbing (we stay climbing)
amafila ife kafunse anzanu
drip drip ngati mvula
chif~kwa chi style ichi nchodhula
ungozindikira ndameta chi mpala
ati nkhiwa uja ndiwa buddha (wa bhudda)
[chorus: brainlock ~tkas]
if you really know me
then you wouldn’t be surprised
daily ndimazisaka sindif~~ka ma guy
thanzi paliponse singasiye kudya nazz
ati ndi ine shasha ndamufunsa wadziwa bwanji?(wadziwa bwanji?)
ati uli ndi drip ngati mvula (ngati mvula) (ayy)
ukakondwa umavuta (ayy)
ex wako amakufuna (ayy)
(iwe) yeah umanjoya opanda chuma (ulibe chuma)
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu kao$forlov3 - pain for all of us
- lirik lagu strokkkin - oldg-
- lirik lagu swavay - baby
- lirik lagu imaginate & eda lovelace - presence
- lirik lagu dj trippie flameboy - dd
- lirik lagu doncare - where i belong
- lirik lagu harpo - humlan
- lirik lagu money kidd - ʎɹɐɯ ʎɯ s,ǝɹǝɥʍ
- lirik lagu god of blood - smile, kids!
- lirik lagu skeletoon - i have the key