lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu brainlock t-kas & nkhiwa - chifwamba

Loading...

[chorus:nkhiwa]
nthawi inayake uzaona ngati wa chifwamba woo
akazakhala ambiri ndimangokhala duu!
they say they won’t copy the things i do
nde zikandibhowa screw screw you
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw

[verse 1 : brainlock t~kas]
nonse manja mwamba ndangofika ndi chi glock
wina asandisegwire we’d phapa’s magazi[?]
5~o ikabwera ife sitimadya runs
popo ndiyokhuta nde chi buns tidyetsa judge
screw screw you and your girlfriend too
wachifwamba wako kaya iwe wati mboom
kwathu ndikufumbi new usadabwe ndilii mbuu!
pano ndine hustler nd~nkatchena ndili ku school
ndangofika usadabwe ine ndichiyabwe
flow yanga ndi mbambande
themba ndi wachabe
yazikwanje nde yake pa beat ndimukhape
skrr sleep n~ggas imudyera babe take
[chorus:nkhiwa]
nthawi inayake uzaona ngati wa chifwamba woah
akazakhala ambiri ndimangokhala duu!
they say they won’t copy the things i do
nde zikandibhowa screw screw you
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw

[verse 2: nkhiwa]
nzakupanga chifwamba iwe screw screw you
flow zanu za plastic ngati nkhuku za dudu
chifwamba chake chomata ngati ndakupakani glue
ma slime ake ndi abodza mumafa tikakufayani doom
ine ndi kas tikafike pamalo nde ndi boom
boys ku spinner chi block imakhala vroom vroom
ndatulukira kwa neighbour
chonde ma guy musanene
chonchi kwa neighbour ayi sindinganene
dumphira kwa neighbour ma guy musanene
chonchili kwa neighbour ayi sindinganene
ndiwakweza ma temper ndiwamvetsa pain
ndiwamvetsa kutentha kenako kugwetsa rain
[chorus:nkhiwa]
nthawi inayake uzaona ngati wa chifwamba woah
akazakhala ambiri ndimangokhala duu!
they say they won’t copy the things i do
nde zikandibhowa screw screw you
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw
screw screw you
screw screw


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...