lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu brainlock boi sticx - kati?

Loading...

[intro]
blxck fyxh i wanna use it as a target

[chorus]
ukubwera ndi kati? ufuna uzindibalalitsa
sindicheza ndi ma yo osati fananiza
ma guy sali mkati amakakamiza
in and out of the city kuthamangitsa mission
ukubwera ndi kati? ufuna uzindibalalitsa
sindicheza ndi ma yo osati fananiza
ma guy sali mkati amakakamiza
in and out of the city kuthamangitsa ma mission

[verse 1]
huh!
couple of weeks back nali zomba ndi ma slime
stuff ili nice wekha tangowona smile
always on the road ngati anandimana bed
kuchoka ku show ku manja kuli ka bread
i’ll take it from here osandipatsa direction
since i was nine i was on a mission
umadziwa yathu ija we in the music business
huh!
we in the music business

[chorus]
ukubwera ndi kati? ufuna uzindibalalitsa
sindicheza ndi ma yo osati fananiza
ma guy sali mkati amakakamiza
in and out of the city kuthamangitsa mission
ukubwera ndi kati? ufuna uzindibalalitsa
sindicheza ndi ma yo osati fananiza
ma guy sali mkati amakakamiza
in and out of the city kuthamangitsa ma mission
[verse 2]
huh
tryna put me in a box but i created this sound
do it straight from my heart
don’t give a f~ck if you down
i ain’t playing this time i swear i’m taking my place
you gon follow my lеad cuz you made a mistake
they keep taking my sound wе gon see how it ends
i was born to create not to follow some trends
i’m a as real as it gets ,i know they never forget
started out in the streets now they see me on tele
what i’m becoming on tele
you don’t put the food in my belly
stop talking sh~t mahn, i’mma just go crazy on em
iwe stop talking bro stop talking
i got this on god

[chorus]
ukubwera ndi kati? ufuna uzindibalalitsa
sindicheza ndi ma yo osati fananiza
ma guy sali mkati amakakamiza
in and out of the city kuthamangitsa mission
ukubwera ndi kati? ufuna uzindibalalitsa
sindicheza ndi ma yo osati fananiza
ma guy sali mkati amakakamiza
in and out of the city kuthamangitsa ma mission

Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...