lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu barry uno - zopanda pake

Loading...

ndine khristu kwambiri kuposa awo
chi khristu changa nacho mnchobeba kuposa chawo
kuchurch kwathu nako nkwabwino kuoosa kwawo
praise team yathuso ndinyatwa kuposa yawo
kwathu amachiza kwawo amangolalika
chopeleka akuchepela ife timahitter mitter
kwathuso timatchena zovala zodhula
fashion timaisata azimayi amaminula
njale zokhazo inu simungamake
otchula ambiriso ndakonko inu simungamake
abusa athu proper pemphero amalitsata
kupemphelela kugwetsa ziwandazo machaka
mulungu amayankha zaoneniko kwathu madalitso kulemela onani abusa athu
anuwo akulenga anuo ndiabodza anuwo ndi afake ndipo alibe chikoka

timangotengeka zinthu zopanda pake
kukomedwa ndizinthu zosangalatsa maso penapake
ziwani ndisatana akugwila ntchito yake
kukongoletsa kuwalitsa zopanda pake
zopanda pake zopanda pake
chenjelani naye ndinjira zakе
zopanda pake zopanda pake
chenjani nayе ndinjira zake

mkazamwalila nane azandiimbile
mwambo uzakhalepo abusa azalalikile
mkazapanga ukwati mpingo uzandiimile
komaso nayo mbiri yanga muzak~mbukile
ena ati kuchenjela ati kuchangamuka akatopa ndiza mdziko huh kukhuzumuka
kubonner zabodza cholinga akufuna banja
sunday lililonse osajomba kukasaka
mpingo uwu amapanga zachikale
ndiwachidhala dhala wachulukaso ndale
kulibe malilime praise ndi worship
kulibekoso band ayi ndikwachimidzi, ena akungotsatilako anzawo
pamene ena akungotsatilako makolo awo
ena ndichikhalidwe sunday samajomba, komaso palibe chomwe iwo amakatola
timangotengeka zinthu zopanda pake
kukomedwa ndizinthu zosangalatsa maso penapake
ziwani ndisatana akugwila ntchito yake
kukongoletsa kuwalitsa zopanda pake
zopanda pake zopanda pake
chenjelani naye ndinjira zake
zopanda pake zopanda pake
chenjani naye ndinjira zake

ambiri mulungu sitimuziwa samasankha ayi ambiri sitiziwa
samaona nkhope maonekedwe koma mtima
samaona tchalitchi koma mkati mwa mtima
kusangalatsa mnzanu zizakupwetekani
zikhulupililo zanu zizakuphwetekani, welengani mawu
kuti mumvetse akuti chani, aneneli onyenga achuluka akupusitsani
angokubelani angokukawani angokuchotsani
akhristu enaso busy kuzuzula anzao kulimbana ndizisoso leka thabwa maso mwao
zolinga zachuluka ndithu chisokonezo kunalembedwa zizaoneka izi k~mapeto
mzimu oyela ali nanu chonde musogozeni
chilungamo mukachiziwa musogozeni

timangotengeka zinthu zopanda pake
kukomedwa ndizinthu zosangalatsa maso penapake
ziwani ndisatana akugwila ntchito yake
kukongoletsa kuwalitsa zopanda pake
zopanda pake zopanda pake
chenjelani naye ndinjira zake
zopanda pake zopanda pake
chenjani naye ndinjira zake
timangotengeka zinthu zopanda pake
kukomedwa ndizinthu zosangalatsa maso penapake
ziwani ndisatana akugwila ntchito yake
kukongoletsa kuwalitsa zopanda pake
zopanda pake zopanda pake
chenjelani naye ndinjira zake
zopanda pake zopanda pake
chenjani naye ndinjira zake


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...