lirik lagu apocalypse - ndachoka kutali
apocalypse – ndachoka kutali feat. saxess
[intro: saxess]
oh ndachoka kutali ineyo, ndachoka kutali ine
lalala lalalala lalalala i’ve come from a far, i’ve come from a far
and i say ebenezer nana ebenezer nana ebenezer nana nanana
[verse 1: apocalypse]
padutsa zaka nyimboyitu ndikulemba
pano nthawi yakwana akwaniritsidwa malemba
people iyi sinyimbo yolalikira i’m not a preacher
ndinyimbo yongothokoza namalenga for i’m his creature
he took me away from the life i was living
i was a dead man living though sometimes i was breathing
i then had a dream i was martin luther king
letting souls run free halleluiah let’s sing
kukhala munthu opanda kanthu ndikudziwa
kukhala nazo zinthu zonse inenso ndikudziwa
ndinali munthu opanda stuff all the way from the gutter
lero ndiyimba ndi chimwemwe yes aladdin, aladdin
[chorus: saxess]
oh kuyimba ndichimwemwe, ndikudziwa
kuvina kuvina nawuwooo, ndikudziwa
poti ndachokera ku ghetto moyo w-nga ah-uh nooh, unasintha
kuyimba ndichimwemwe nawooh, kuvina vina vina nawooh
moyo w-nga have come from a far
god has brought me this far
[verse 2: apocalypse]
zinanditengera zaka six ndinso theka
zomwe sizitheka ndiifeyo ndi ambuye ndizotheka
usiku unatalika nyali inayamba kuzima
zoona zinthu zinkavuta komabe osataya mtima
i’m going steady to the promised land hard boy
ready to discover what’s behind the closed doors yo
it only has begun mic check you know the drill uh
ambuye akachiyamba chinthu inu samachisiya
you know ndikutali ndikupita
ndani angandibweze palibe nkutali ndachokera
every breath that i’m taking, bars that i’m dropping
i wana let them people know it’s all about you jesus
[chorus: saxess]
oh kuyimba ndichimwemwe, ndikudziwa
kuvina kuvina nawuwooo, ndikudziwa
poti ndachokera ku ghetto moyo w-nga ah-uh nooh, unasintha
kuyimba ndichimwemwe nawooh, kuvina vina vina nawooh
moyo w-nga have come from a far
god has brought me this far
[verse 3: apocalypse]
pamapeto anthu akandiona amati chani? thoka
nanga inuyo mukandionamumati ndine yani? apoca
yes ndine apoca chaplain oyimba uja
ngakhaletu sometimes think only god knows me
the day like today make the devil wana take a breath away
to him what a shame cause my god ain’t no blind
oh no no no oh no
and them people have a say to justify my claim yes
so i stand up for them unheard voices
sindidzakhala chete no sindidzagona
mpaka tsiku lodzavala pakhosi w-nga kolona yes
[chorus: saxess]
oh kuyimba ndichimwemwe, ndikudziwa
kuvina kuvina nawuwooo, ndikudziwa
poti ndachokera ku ghetto moyo w-nga ah-uh nooh, unasintha
kuyimba ndichimwemwe nawooh, kuvina vina vina nawooh
moyo w-nga have come from a far
god has brought me this far
[outro: apocalypse]
sometimes when we saying that you know the drill, this, that, people just think it’s whatsoever
but mayne making this type of song doesn’t mean i’m perfect, doesn’t mean i have it all
komabe it’s just tryna be respectful, grateful to god for all the things he has done mayne
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu olltii - 담배 (cigarette)
- lirik lagu pride - zuhältertape 2 imitation
- lirik lagu finder - протест
- lirik lagu john garcia - kylie
- lirik lagu the mouseketeers - mickey mouse march (from "club mickey mouse")
- lirik lagu les dales hawerchuk - abuse de moé
- lirik lagu robert hazard - route 666
- lirik lagu diddi trix - la maille
- lirik lagu zitro - day job
- lirik lagu 96ix - love me back