![lirik.web.id](https://lirik.web.id/tema/logo.png)
lirik lagu alick macheso - kunditaya
[intro: jonas kasamba]
al!ck macheso, agitate of sungura, atomic bomba
[verse 1: al!ck macheso]
abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
abambo anga inu, zomwe munapanga sizinthu zabwino ndithu
ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii
ndizabwino kwainuyo, koma kwaine sizomwe, chimodzimodzi ndi amayii w~nga oooo
[verse 2: al!ck macheso]
kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
kunditaya, kunditaya, kunditayira mudzenje abambo anga ine ndithu
kunditaya, kunditaya, kunditayira muchitini abambo anga ine ndithu
[verse 3: al!ck macheso]
kunditayirira ine ngati mbuzi ine, abambo anga mulibe chisoni
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
munandibalira umphawi ineyo, kundibalira umphawii
[chorus: al!ck macheso]
abambo anga ine (abambo anga ine), umoyo w~nga ine (umoyo w~nga ine), wokulira muumphawi (wokulira muumphawi), ndine mwana wa masiye ine (ndine mwana wa masiye ine)
zomvetsa chisoni, ndithu siumoyo wosangalatsaa
[outro: al!ck macheso]
ndilibe chomwe ndingapange ineyo chif~kwa ndine mwana
chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
(abambo anga inee ndithu)
ndilibe chomwe ndingapange ineyo chif~kwa ndine mwana
chimene chinakupatsani kuti mupange zimenezi
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu greatwaterpressure - passo zero
- lirik lagu kaylee hazel - thinking bout you
- lirik lagu üçkuruş - zamansız buseler (feat. selen özel)
- lirik lagu jonny october - goongala!
- lirik lagu 6soundz (svk) - yellow❗
- lirik lagu m$ny - making bank
- lirik lagu young knives - the people from the second way
- lirik lagu sylvie vartan - j'ai deux mains, j'ai deux pieds, une bouche et puis un nez
- lirik lagu драка тёлок (draka tyolok) & august246 - юрий лоза (yuriy loza)
- lirik lagu ovi wood - the way i love u