lirik lagu afana ceez feat. leslie - konde
tiye tiyambe
aye aye yeah
aye aye
nawe umandiyimilila ndikakhala pansi
umandichotsa ludzu ndikafuna madzi
ndiwe sindidzasowa kanthu
eish kunyadilana, kunyadilana
kupatsilana chimwemwe mosawuzana
kudalirana, kugawilana
kugawilana chikondi mosamanana eish
zomwe unalakwitsa ndi za make dzana
zomwe ndimalakwa umazipambana
kundiyimilila olo utangokhala
sindikuvala koma ase umandikhala
umandikhala nawe ndimakukhala
ineyo mpando wako ndipo umandikhala
mtima w~nga kwa iweyo ndinamwaza
zoswelanaso mtima tinakanizana ndiye
ponda apo nane ndiponde apa
gwila apo nane ndikugwile apa
tivine stepe yokamanga wa muyaya
adziwe ndine wako iweso ndi w~nga
tizikondana baby timakondana baby
iwe ndi w~nga bae
ndiye undikonde konde konde
ndiye undikonde konde konde
you are my favourite boy
kunamizana kunamizana
k~mathawana k~mbali tikufilana
kuzembelana mwa bodza ngati ana
kung′alula kuli kuwopa undikana koma
pano takula tasiya zachibwana
pano ndagula mphete kuti ukhale w~nga
kulonjezana kulonjezana
pa makolo kuti sitizasiyana dziwa
zomwe unalakwitsa ndi za make dzana
iyi ikhale banja ndipo ukhale make wana
umandiyimilila olo utangokhala
zonse umakhumba nzakupatsa ine apa ndiye
ponda apo nane ndiponde apa
gwila apo nane ndikugwile apa
tivine stepe yokamanga wa muyaya
adziwe ndine wako iweso ndi w~nga
tizikondana baby timakondana baby
iwe ndi w~nga bae
ndiye undikonde konde konde
ndiye undikonde konde konde
you are my favourite boy
give me loving on a daily
undikonde konde konde
nawe umandiyimilila ndikakhala pansi
umandichotsa ludzu ndikafuna madzi
ndiwe sindizasowa kanthu
ndiye ponda apa nane ndiponde apo
gwila apa nane ndikugwile apo
ponda apa nane ndiponde apo
gwila apa nane ndikugwile apo
tizikondana baby timakondana baby
iwe ndi w~nga bae
ndiye undikonde konde konde
ndiye undikonde konde konde
you are my favourite boy
give me loving on a daily
undikonde konde konde
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu draag me - faces of vultures
- lirik lagu wi$ard - tower of babble
- lirik lagu toure - tied in
- lirik lagu video days - bed
- lirik lagu praisexxme - shit i been on lately
- lirik lagu sin icon - d3cay
- lirik lagu pabs aka - vuelo pa brasil
- lirik lagu lil jeffy - hit it
- lirik lagu mxrvxlll - armageddon
- lirik lagu observerr - curse