
lirik lagu ace dirty - polar
[intro: crispy malawi]
ndufuna dollar
ngini yako sili sharp ngati mpeni wosanola
ndili pa easy kuyiwerenga game sizoti ndangopola
ndimasuta ma grams baby sindisuta bhola
[chorus: crispy malawi]
yeah b~tch don’t get too comfortable
ngati wabwera lero ndekut upite leronso
grab your phone and keep it on the low
ndiku caller ndikakufuna koma apa ndi chase kaye dollar
ndiku chaser dollar ine ndikufuna dollar
ngini yako sili sharp ngati mpeni wosanola
ndili pa easy kuyiwerenga game sizoti ndangopola
ndimasuta ma grams baby sindisuta bhola
[verse 1: crispy malawi]
awa ndima swazi sicha nkhotakota
samatha ku roller k~mangogula chopota pota
timakonda ku chaser tatopa ndizolota lota
umakonda milandu utha k~muvktera walter
nde what it do fam? tiku runner d~nkam
sk!ll yosabeleka tiyifunse fipam
[verse 2]
mfana wa short temper ndipo zangondilemba
yama go getter kupusha swazi kutheba
ndili ndi spe chaku chinsapo
high ngati mitambo
apa kandifikapo, please don’t get too comfortable
usatase, ndikufuna kuka hassa
ndungofuna kuphaka ngati ndi kuwopa ku gasser
osawuza fans zomwe timapangazi
she’s a freak in the sheets in the streets ndikamanyazi
[chorus: crispy malawi]
yeah b~tch don’t get too comfortable
ngati wabwera lero ndekut upite leronso
grab your phone and keep it on the low
ndiku caller ndikakufuna koma apa ndi chase kaye dollar
ndiku chaser dollar ine ndikufuna dollar
ngini yako sili sharp ngati mpeni wosanola
ndili pa easy kuyiwerenga game sizoti ndangopola
ndimasuta ma grams baby sindisuta bhola
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu nanaupsidedown - i can't hear you
- lirik lagu xema fuentes, arzadous & carla frigo - mr. saxobeat
- lirik lagu gpc - hand drauf
- lirik lagu zewei - yhngnyem
- lirik lagu 114hz - wazabi
- lirik lagu teo lucadamo - buen día
- lirik lagu argentina - a grandeza do fado
- lirik lagu saturnalias - toys r sus
- lirik lagu vyka - one of many
- lirik lagu ynkeumalice - culver’s and chill