
lirik lagu 6th mw - ayi (bad energy)
[intro]
yeah, yeah
ayo landie, this one about
[chorus: 6th]
no bad energy (zimenezo ayi)
osamvera enemy (zimenezo ayi)
no bad energy (zimenezo ayi)
osamvera enemy (zimenezo ayi)
amafuna atigwetse
iwe ndi ine atisiyanitse
awa amakonda miseche
ukawawona umafunika uwapewe
amafuna atigwetse
iwe ndi ine atisiyanitse
awa amakonda miseche
ukawawona kufunika uwapewe
[verse 1 :6th]
stay focused never lose hope
nuffa dem wanna see you flow
another day man a still wake up
make a month never give up
awa amafuna atisokoneze
tikamapita kufuna atibweze
ma buku mwawo azatilembe
pa mawa awa azatilekeze
achina jorgina, maria ena amawasilira
pomwe tinafika ~n~lowelera sadziwa komwe akupita
[chorus: 6th]
no bad energy (zimenezo ayi)
osamvera enemy (zimenezo ayi)
no bad energy (zimenezo ayi)
osamvera enemy (zimenezo ayi)
amafuna atigwetse
iwe ndi ine atisiyanitse
awa amakonda miseche
ukawawona umafunika uwapewe
amafuna atigwetse
iwe ndi ine atisiyanitse
awa amakonda miseche
ukawawona kufunika uwapewe
[verse 2: brainlock t~kas]
ay, pena ndimapusa koma sindingavomereze
usandikwiyire tandisekelere
ndibwera kwanu ndufuna ndikunyengelere
ma kape chimwemwe afuna atibele
ndufuna ndibwere kwanu ndizakutenge
ndi kale lija ndikufuna ticheze
bad energy ku mixer ndima fake friends
ma opp n~gga mpata asawupeze
crazy how we got this far baby
they put us in the dark now we shine baby
nde uzichenjera ndi obwera cha mpeni
bad energy stay away from me
[chorus: 6th]
no bad energy (zimenezo ayi)
osamvera enemy (zimenezo ayi)
no bad energy (zimenezo ayi)
osamvera enemy (zimenezo ayi)
amafuna atigwetse
iwe ndi ine atisiyanitse
awa amakonda miseche
ukawawona umafunika uwapewe
amafuna atigwetse
iwe ndi ine atisiyanitse
awa amakonda miseche
ukawawona kufunika uwapewe
[outro: krazie g]
we ain’t got no time
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu mph - pre's
- lirik lagu megaloh - bully
- lirik lagu mariek - point of view
- lirik lagu downgr4de - panacea of indifference
- lirik lagu 青木陽菜 (hina aoki) - colors of you
- lirik lagu ati242, uzi & batuflex - khrbr (original release)
- lirik lagu mr. john deway - jamais t'oublie
- lirik lagu swya - why
- lirik lagu czesław niemen - marionetki
- lirik lagu souljahpino - acostumado a falar na terceira pessoa